Yohane 9:30 BL92

30 Munthuyu anayankha nati kwa iwo, Pakuti cozizwa ciri m'menemo, kuti inu simudziwa kumene acokera, ndipo ananditsegulira maso anga.

Werengani mutu wathunthu Yohane 9

Onani Yohane 9:30 nkhani