Yohane 9:31 BL92

31 Tidziwa kuti Mulungu samvera ocimwa. Koma ngati munthu ali yense akhala wopembedza Mulungu nacita cifuniro cace, amvera ameneyo.

Werengani mutu wathunthu Yohane 9

Onani Yohane 9:31 nkhani