31 ndi kucipululu, kumene munapenya kuti Yehova Mulungu wanu anakunyamulani, monga anyamula mwana wace wamwamuna, m'njira monse munayendamo, kufikira mutalowa m'malo muno.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1
Onani Deuteronomo 1:31 nkhani