Deuteronomo 1:4 BL92

4 atakantha Sihoni mfumu ya Aamori, wakukhala m'Hesiboni, ndi Ogi mfumu ya Basana, wakukhala m'Asitaroti, ku Edrei.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1

Onani Deuteronomo 1:4 nkhani