4 Ndipo analembera pamagome, monga mwa malembedwe oyamba, mau khumiwo, amene Yehova adanena ndi inu m'phirimo, ali pakati pa moto, tsiku la kusonkhanako; ndipo Yehova anandipatsa awa.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 10
Onani Deuteronomo 10:4 nkhani