Deuteronomo 12:14 BL92

14 koma pamalo pamene Yehova adzasankha, mwa limodzi la mapfuko anu, pamenepo muzipereka nsembe zanu zopsereza, ndi pamenepo muzicita zonse ndikuuzani.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:14 nkhani