7 ndipo kumeneko muzidya pamaso pa Yehova Mulungu wanu, ndi kukondwera nazo zonse mudazigwira ndi dzanja lanu, inu ndi a pa banja lanu, m'mene Yehova Mulungu wanu anakudalitsani.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12
Onani Deuteronomo 12:7 nkhani