Deuteronomo 14:21 BL92

21 Musamadya cinthu ciri conse citafa cokha; muzipereka ico kwa mlendo ali m'mudzi mwanu, acidye ndiye; kapena ucigulitse kwa mlendo; popeza ndinu mtundu wa anthu wopatulika wa Yehova Mulungu wanu. Musamaphika mwana wa mbuzi mu mkaka wa mace.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 14

Onani Deuteronomo 14:21 nkhani