2 Cilekereroco ndici: okongoletsa onse alekerere cokongoletsa mnansi wace; asacifunse kwa mnansi wace, kapena mbale wace; popeza analalikira cilekerero ca Yehova.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 15
Onani Deuteronomo 15:2 nkhani