Deuteronomo 15:5 BL92

5 cokhaci mumvere cimverere mau a Yehova Mulungu wanu, kuti musamalire kucita malamulo awa onse amene ndikuuzani lero lino.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 15

Onani Deuteronomo 15:5 nkhani