Deuteronomo 16:1 BL92

1 Samalirani mwezi wa Abibu, kuti muzicitira Yehova Mulungu wanu Paskha; popeza m'mwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakuturutsani m'dziko la Aigupto usiku.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16

Onani Deuteronomo 16:1 nkhani