Deuteronomo 16:13 BL92

13 Mudzicitire madyerero a misasa masiku asanu ndi awiri, mutasunga za padwale ndi za mopondera mphesa;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16

Onani Deuteronomo 16:13 nkhani