19 Musamapotoza ciweruzo, musamasamalira munthu, kapena kulandira cokometsera mlandu; popeza cokometsera mlandu cidetsa maso a anzeru, niciipsa mau a olungama.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16
Onani Deuteronomo 16:19 nkhani