8 Masiku asanu ndi limodzi muzidya mkate wopanda cotupitsa; ndipo tsiku lacisanu ndi ciwiri ndilo loletsa, la Yehova Mulungu wanu; musamagwira nchito pamenepo.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16
Onani Deuteronomo 16:8 nkhani