1 Musamaphera Yehova Mulungu wanu nsembe ya ng'ombe, kapena nkhosa, yokhala naco cirema, kapena ciri conse coipa; pakuti cinyansira Yehova Mulungu wanu.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 17
Onani Deuteronomo 17:1 nkhani