14 Mutakalowa m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani, ndi kulilandira lanu lanu, ndi kukhalamo; ndipo mukanena, Tidziikire mfumu, monga amitundu onse akutizinga;
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 17
Onani Deuteronomo 17:14 nkhani