16 Koma asadzicurukitsire akavalo iye, kapena kubwereretsa anthu amke ku Aigupto, kuti acurukitse akavalo; popeza Yehova anati nanu, Musamabwereranso njira iyi.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 17
Onani Deuteronomo 17:16 nkhani