7 Liyambe kumgwera dzanja la mboniyo kumupha; pamenepo dzanja la anthu onse, Potero muzicotsa coipaco pakati panu.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 17
Onani Deuteronomo 17:7 nkhani