Deuteronomo 18:10 BL92

10 Asapezeke mwa inu munthu wakupitiriza mwana wace wamwamuna kapena mwana wace wamkazi ku mota wa ula, wosamalira mitambo, kapena wosamalira kulira kwa mbalame, kapena wanyanga.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 18

Onani Deuteronomo 18:10 nkhani