Deuteronomo 18:12 BL92

12 Popeza ali yense wakucita izi Yehova anyansidwa naye; ndipo cifukwa ca zonyansa izi Yehova Mulungu wanu awapitikitsa pamaso panu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 18

Onani Deuteronomo 18:12 nkhani