Deuteronomo 18:18 BL92

18 Ndidzawaukitsira mneneri wa pakati pa abale ao, wonga iwe; ndipo ndidzampatsa mau anga m'kamwa mwace, ndipo adzanena nao zonse ndimuuzazi.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 18

Onani Deuteronomo 18:18 nkhani