20 Koma mneneri wakucita modzikuza ndi kunena mau m'dzina langa, amene sindinamlamulira anene, kapena kunena m'dzina la milungu yina, mneneri ameneyo afe.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 18
Onani Deuteronomo 18:20 nkhani