22 Mneneri akanena m'dzina la Yehova, koma mau adanenawa sacitika, nisafika, ndiwo mau Yehova sanawanena; mneneriyo ananena modzikuza, musamuopa iye.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 18
Onani Deuteronomo 18:22 nkhani