Deuteronomo 18:3 BL92

3 Ndipo zoyenera ansembe, awapatse anthu akuphera nsembe ndizo: ingakhale ng'ombe kapena nkhosa azipatsa wansembe mwendo wamwamba, ndi ya m'masaya ndi chipfu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 18

Onani Deuteronomo 18:3 nkhani