Deuteronomo 19:17 BL92

17 pamenepo anthu onse awiri, pakati pao pali makaniwo, aziima pamaso pa Yehova, pamaso pa ansembe ndi oweruza okhala m'masiku awa;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 19

Onani Deuteronomo 19:17 nkhani