Deuteronomo 19:3 BL92

3 Mudzikonzere njira, ndi kugawa malire a dziko lanu, limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale lanu lanu, patatu; kuti wakupha munthu athawireko.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 19

Onani Deuteronomo 19:3 nkhani