Deuteronomo 19:6 BL92

6 kuti wolipsa mwazi angalondole wakupha mnzace, pokhala mtima wace watentha, nampeza, popeza njira njaitali, namkantha kuti wafa; angakhale sanaparamula imfa, poona sanamuda kale lonse.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 19

Onani Deuteronomo 19:6 nkhani