Deuteronomo 2:12 BL92

12 Ndipo Ahori anakhala m'Seiri kale, koma ana a Esau analanda dziko lao, nawaononga pamaso pao, nakhala m'malo mwao; monga Israyeli anacitira dziko lace lace, limene Yehova anampatsa.)

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 2

Onani Deuteronomo 2:12 nkhani