34 Ndipo muja tinalanda midzi yace yonse; ndipo tinaononga konse midzi yonse, amuna ndi akazi ndi ana; sitinasiyapo ndi mmodzi yense.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 2
Onani Deuteronomo 2:34 nkhani