16 Koma za midzi ya amitundu awa, imene Yehova Mulungu wanu akupatsani, ikhale colowa canu, musasiyepo camoyo ciri conse cakupuma;
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 20
Onani Deuteronomo 20:16 nkhani