5 Ndipo akapitao anene ndi anthu, ndi kuti, Ndani munthuyo anamanga nyumba yatsopano, osalowamo? amuke nabwerere kunyumba kwace, kuti angafe kunkhondo nangalowemo munthu wina.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 20
Onani Deuteronomo 20:5 nkhani