1 Akapeza munthu waphedwa m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale lanu lanu, nagona pamunda, wosadziwika wakumkantha,
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 21
Onani Deuteronomo 21:1 nkhani