8 Landirani, Yehova, cotetezera anthu anu Israyeli, amene munawaombola, ndipo musalole mwazi wosacimwa ukhale pakati pa anthu anu Israyeli; ndipo adzawatetezera ca mwaziwo.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 21
Onani Deuteronomo 21:8 nkhani