29 pamenepo mwamuna amene anagona naye azipatsa atate wace wa namwaliyo masekeli makumi asanu a siliva, ndipo azikhala mkazi wace; popeza anamcepetsa; sakhoza kumcotsa masiku ace onse.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 22
Onani Deuteronomo 22:29 nkhani