Deuteronomo 23:24 BL92

24 Mukalowa m'munda wamphesa wa mnansi wanu, mudyeko mphesa ndi kukhuta nazo monga mufuna eni koma musaika kanthu m'cotengera canu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 23

Onani Deuteronomo 23:24 nkhani