3 M-amoni kapena Mmoabu asalowe m'msonkhano wa Yehova; ngakhale mbadwo wao wakhumi usalowe m'msonkhano wa Yehova, ku nthawi zonse;
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 23
Onani Deuteronomo 23:3 nkhani