5 Ndipo Yehova Mulungu wanu sanafuna kumvera Balamu; koma Yehova Mulungu wanu anakusandulizirani tembererolo likhale mdalitso, popeza Yehova Mulungu wanu anakukondani.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 23
Onani Deuteronomo 23:5 nkhani