Deuteronomo 24:1 BL92

1 Munthu akatenga mkazi akhale wace, kudzali, ngati sapeza ufulu pamaso pace, popeza anapeza mwa iye kanthu kosayenera, amlembere kalata wa cilekanitso, ndi kumpereka uyu m'dzanja lace, ndi kumturutsa m'nyumba mwace.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 24

Onani Deuteronomo 24:1 nkhani