Deuteronomo 24:14 BL92

14 Musamasautsa wolembedwa nchito, wakukhala waumphawi ndi wosauka, wa abale anu kapena wa alendo ali m'dziko mwanu, m'midzi mwanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 24

Onani Deuteronomo 24:14 nkhani