Deuteronomo 25:15 BL92

15 Muzikhala nao mwala wa muyeso wofikira ndi woyenera; mukhale nao muyeso wa efa wofikira ndi woyenera; kuti masiku anu acuruke m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 25

Onani Deuteronomo 25:15 nkhani