Deuteronomo 26:3 BL92

3 Ndipo mufike kwa wansembe wakukhala m'masiku awa, ndi kunena naye, Ndibvomereza lero lino kwa Yehova Mulungu wako, kuti ndalowa m'dziko limene Yehova analumbirira makolo athu, kuti adzatipatsa ili.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 26

Onani Deuteronomo 26:3 nkhani