Deuteronomo 28:1 BL92

1 Ndipo kudzali, mukadzamvera mau a Yehova Mulungu wanu mwacangu, ndi kusamalira kucita malamulo ace onse amene ndikuuzani lero, kuti Yehova Mulungu wanu adzakukulitsani koposa amitundu onse a pa dziko lapansi;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 28

Onani Deuteronomo 28:1 nkhani