Deuteronomo 28:11 BL92

11 Ndipo Yehova adzakucurukitsirani zokoma, m'zipatso za thupi lanu, ndi m'zipatso za zoweta zanu, ndi m'zipatso za nthaka yanu, m'dziko limene Yehova analumbirira makolo anu kuti adzakupatsani ilo,

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 28

Onani Deuteronomo 28:11 nkhani