21 Yehova adzakumamatiritsani mliri kufikira akakuthani kukucotsani kudziko, kumene mupitako kulilandira.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 28
Onani Deuteronomo 28:21 nkhani