Deuteronomo 28:35 BL92

35 Yehova adzakukanthani ndi cironda coipa cosacira naco kumaondo, ndi kumiyendo, kuyambira pansi pa phazi lanu kufikira pamwamba pa mutu panu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 28

Onani Deuteronomo 28:35 nkhani