Deuteronomo 28:56 BL92

56 Mkazi wololopoka nkhongono ndi wanyonga pakati pa inu, wosayesa kuponda pansi ndi phazi lace popeza ndiye wanyonga, ndi wololopoka nkhongono, diso lace lidzamuipira mwamuna wa pamtima pace, ndi mwana wace wamwamuna ndi wamkazi;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 28

Onani Deuteronomo 28:56 nkhani