Deuteronomo 28:63 BL92

63 Ndipo kudzali kuti, monga Yehova anakondwera nanu kukucitirani zabwino, ndi kukucurukitsani; momwemo Yehova adzakondwera nanu kutayikitsa ndi kuononga inu, ndipo adzakuzulani kudziko kumene mulowako kulilandira.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 28

Onani Deuteronomo 28:63 nkhani