2 Ndipo Yehova anati kwa ine, Usamuopa; popeza ndampereka iye ndi anthu ace onse, ndi dziko lace, m'dzanja lako; umcitire monga umo unacitira Sihoni mfumu ya Aamori, amene anakhala m'Hesiboni.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 3
Onani Deuteronomo 3:2 nkhani