5 ndipo Yehova Mulungu wanu adzakulowetsani m'dziko lidakhala lao lao la makolo anu, nilidzakhala lanu lanu; ndipo adzakucitirani zokoma, ndi kukucurukitsani koposa makolo anu.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 30
Onani Deuteronomo 30:5 nkhani