Deuteronomo 30:8 BL92

8 Pamenepo mutembenuke ndi kumvera mau a Yehova, ndi kucita malamulo ace onse amene ndikuuzani lero lino.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 30

Onani Deuteronomo 30:8 nkhani